Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli ananena ndi Ahiya, Bwera nalo likasa la Mulungu kuno. Pakuti likasa la Mulungu linali kumeneko masiku aja ndi ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:18 nkhani