Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onse awiri anadziulula kwa a ku kaboma ka Afilistiwo; ndipo Afilistiwo anati, Onani, Ahebri alikuturuka m'mauna m'mene anabisala.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:11 nkhani