Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali kuti pakutsiriza iye kupereka nsembe yopserezayo, pomwepo, onani, Samueli anafika. Ndipo Sauli anamcingamira kukamlankhula iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:10 nkhani