Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 12:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse ananena ndi Samueli, Mupempherere akapolo anu kwa Yehova Mulungu wanu, kuti tingafe; popeza pamwamba pa zoipa zathu zonse tinaonjeza coipa ici, cakuti tinadzipemphera mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:19 nkhani