Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 12:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Samueli anaitana kwa Yehova; ndipo Yehova anatumiza bingu ndi mvula tsiku lomwelo; ndipo anthu onse anaopa kwambiri Yehova ndi Samueli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:18 nkhani