Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukaopa Yehova ndi kumtumikira ndi kumvera mau ace, ndi kusakana lamulo lace la Yehova, ndipo inu ndi mfumu imene iweruza inu mukadzatsata Yehova Mulungu wanu, cabwino.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:14 nkhani