Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 11:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse anapita ku Giligala; ndi kumeneko analonga Sauli mfumu pamaso pa Yehova m'Giligala; ndi pamenepo anaphera nsembe zoyamika pamaso pa Yehova; ndi pomwepo Sauli ndi anthu onse a Israyeli anakondwera kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 11

Onani 1 Samueli 11:15 nkhani