Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukapitirira pamenepo tsono ndi kufika ku mtengo wathundu wa ku Tabori, kumeneko adzakomana nanu anthu atatu akukwera kwa Mulungu ku Beteli, wina wonyamula ana a mbuzi atatu, wina mikate itatu, wina thumba la vinyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:3 nkhani