Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mene talekana lero, mudzakomana ndi anthu awiri pa manda a Rakele, pa malire a Benjamini ku Zeliza; iwo ndiwo adzanena nanu, Aburu aja munakafuna, anapezedwa; ndipo onani, atate wanu analeka kulingalira aburuwo, koma alikulingalira za inu, ndi kuti, Ndidzacita ciani, cifukwa ca mwana wanga?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:2 nkhani