Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, kuti onse amene anamdziwiratu kale, pakuona ici cakuti, onani, iye ananenera pamodzi ndi aneneri, anati wina ndi mnzace, Ici nciani cinamgwera mwana wa Kisi? Kodi Saulinso ali mwa aneneri?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:11 nkhani