Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 1:27-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Ndinampempha mwanayu; ndipo Yehova anandipatsa copemphacanga ndinacipempha kwa iye;

28. cifukwa cace inenso ndinampereka kwa Yehova; masiku onse a moyo wace aperekedwa kwa Yehova. Ndipo analambira Yehova pomwepo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1