Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 1:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkaziyo ananena, Mbuye wanga, pali moyo wanu, zoonadi ine ndine mkazi uja ndidaima pano ndi inu, ndi kupemphera kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:26 nkhani