Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Rubeni mwana woyamba wa Israyeli, (pakuti ndiye mwana woyamba; koma popeza anaipsa kama wa atate wace ukulu wace unapatsidwa kwa ana a Yosefe mwana wa Israyeli, koma m'buku la cibadwidwe asayesedwe monga mwa ukulu wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 5

Onani 1 Mbiri 5:1 nkhani