Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 29:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamphera Yehova nsembe, napereka nsembe zopsereza kwa Yehova m'mawa mwace mwa tsiku lija, ndizo ng'ombe cikwi cimodzi, nkhosa zamphongo cikwi cimodzi, ndi ana a nkhosa cikwi cimodzi, pamodzi ndi nsembe zao zothira, ndi nsembe zocuruka za Aisrayeli onse:

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:21 nkhani