Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 29:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa khamu lonse, Mulemekeze tsono Yehova Mulungu wanu. Ndi khamu lonse linalemekeza Yehova Mulungu wa makolo ao, nawerama, nalambira Yehova, ndi mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:20 nkhani