Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 27:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wacisanu ndi cimodzi wa mwezi wacisanu ndi cimodzi ndiye Ira mwana wa Ikesi Mtekoi; ndi m'cigawo mwace zikwi makumi awiri mphambu zinai.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27

Onani 1 Mbiri 27:9 nkhani