Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 25:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ciwerengo cao, pamodzi ndi abale ao ophunzitsidwa ayimbire Yehova, onse anthetemya, ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 25

Onani 1 Mbiri 25:7 nkhani