Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 25:12-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. wacisanu Netaniya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;

13. wacisanu ndi cimodzi Bukiya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;

14. wacisanu ndi ciwiri Yesarela: ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;

15. wacisanu ndi citatu Yesaya, ana ace ndi abale ace khumi ndi awiri;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 25