Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 22:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Perekani tsono mtima ndi moyo wanu kufunafuna Yehova Mulungu wanu; ndipo nyamukani ndi kumanga malo opatulika a Yehova Mulungu, kuti abwere nalo likasa la cipangano la Yehova, ndi zipangizo zopatulika za Mulungu, ku nyumba imene idzamangidwira dzina la Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 22

Onani 1 Mbiri 22:19 nkhani