Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 20:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naturutsanso anthu anali m'mwemo, nawaceka ndi mipeni ya mana mano, ndi zipangizo zocekera zacitsulo, ndi nkhwangwa. Anatero Davide ndi midzi yonse ya ana a Amoni. Ndipo Davide ndi anthu onse anabwera ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 20

Onani 1 Mbiri 20:3 nkhani