Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 19:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akalonga a ana a Amoni anati kwa Hanuni, Davide ali kucitira atate wanu ulemu kodi, popeza anakutumizirani otonthoza? sakudzerani kodi anyamata ace kufunafuna, ndi kugubuduza, ndi kuzonda dziko?

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19

Onani 1 Mbiri 19:3 nkhani