Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 19:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitatha izi, Nahasi mfumu ya ana a Amoni anamwalira, ndi mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19

Onani 1 Mbiri 19:1 nkhani