Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 12:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anaturuka kukomana nao, nayankha, nanena nao, Ngati mwandidzera mwamtendere kundithandiza, mtima wanga udzalumikizana nanu; koma ngati mwafika kundipereka kwa adani anga, popeza m'manja mwanga mulibe ciwawa, Mulungu wa makolo athu acione ndi kucilanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:17 nkhani