Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 9:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu yense wopitirira pa nyumba yaitali yino adzadabwa nayo, nadzainyoza, nadzati, Yehova watero cifukwa ninji ndi dziko lino ndi nyumba yino?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:8 nkhani