Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 9:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Solomo anamanga zombo zambiri ku Ezioni Geberi uli pafupi ndi Eloti, pambali pa Nyanja Yofiira, ku dziko la Edomu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:26 nkhani