Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza Hiramu mfumu ya Turo adamthandiza Solomo ndi mitengo yamkungudza ndi yamlombwa ndi golidi yemwe, monga momwe iye anafuniramo, cifukwa cace mfumu Solomo anampatsa Hiramu midzi makumi awiri m'dziko la Galileya.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:11 nkhani