Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo akabwerera kwa Inu ndi mtima wao wonse ndi moyo wao wonse, m'dziko la adani ao adawatenga ndendewo, ndipo akapemphera kwa Inu molunjika ku dziko lao munapatsa makolo aolo, ku mudzi munausankha Inu, ndi kunyumba ndamangira dzina lanu;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:48 nkhani