Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo mverani Inu m'Mwamba mokhala Inu, ndi kukhululukira, ndi kucita, ndi kubwezera munthu yense monga njira zace zonse, amene Inu mumdziwa mtima wace, popeza Inu, Inu nokha, mudziwa mitima ya ana onse a anthu;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:39 nkhani