Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

tsono pempho ndi pembedzero liri lonse akalipempha munthu ali yense, kapena anthu anu onse Aisrayeli, pakuzindikira munthu yense cinthenda ca mtima wa iye yekha, ndi kutambasulira manja ace ku nyumba yino;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:38 nkhani