Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mverani Inu pamenepo m'mwambamo, ndipo citani, weruzani akapolo anu, kumtsutsa woipayo, ndi kumbwezera cimo lace, ndi kulungamitsa wolungamayo kumbwezera monga cilungamo cace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:32 nkhani