Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati munthu akacimwira mnzace, ndi lumbiro likaikidwa pa iye kumlumbiritsa, ndipo akadzalumbira patsogolo pa guwa la nsembe lanu m'nyumba yino;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:31 nkhani