Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, Yehova Mulungu wa Israyeli, msungireni mtumiki wanu Davide atate wanga cimene cija mudamlonjezaco, ndi kuti, Sadzakusowa munthu pamaso panga wokhala pa mpando wacifumu wa Israyeli; komatu ana ako acenjere njira yao, kuti akayende pamaso panga monga umo unayendera iwe pamaso panga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:25 nkhani