Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Solomo anasonkhanitsa akulu a Israyeli, ndi akulu onse a mafuko, akalonga a nyumba za atate a ana a Israyeli, kwa mfumu Solomo m'Yerusalemu, kukatenga likasa la cipangano ca Yehova m'mudzi wa Davide, ndiwo Ziyoni.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:1 nkhani