Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anapanga zipangizo zonse za m'nyumba ya Mulungu: guwa la nsembe lagolidi, ndi gome lagolidi loikapo mikate yoonekera;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:48 nkhani