Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga mbiya zamphwamphwa khumi zamkuwa; m'mbiya imodziyo munalowamo madzi a mitsuko yaikuru makumi anai, ndipo mbiya iri yonse inali ya mikono inai: pa phaka liri lonse la maphaka aja khumi panakhala mbiya imodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:38 nkhani