Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo njinga zinai zinali pansi pa matsekerezo, ndi mitanda ya njinga inali m'mphakamo, ndi msinkhu wa njinga imodzi unali mkono umodzi ndi nusu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:32 nkhani