Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakamwa pace m'katimo pamwamba pa cosanjikira, panayesa mkono umodzi; koma pakamwa pace panali posadamuka, monga mapangidwe ace a cosanjikira, mkono umodzi ndi nusu; ndiponso pakamwa pace panali zolemba ndi matsekerezo ace anali amphwamphwa, si ozunguniza.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:31 nkhani