Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'khosi mwace munali ngati zikho zozinganiza m'mkono umodzi zikho khumi zakuzinganiza thawalelo; zikhozo zinayengedwa m'mizere iwiri poyengedwa thawalelo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:24 nkhani