Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 6:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Khomo lolowera m'zipinda za pakati linali ku mbali ya ku dzanja lamanja ya nyumba; ndipo anthu amakwerera pa makwerero ozunguniza, kutikira ku zipinda za pakati, ndi kuturuka m'zapakatizo kulowa m'zacitatuzo,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:8 nkhani