Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 6:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cipinda capansico kupingasa kwace kunali mikono isanu, capakatico kupingasa kwace mikono isanu ndi umodzi, cacitatuco kupingasa kwace mikono isanu ndi iwiri; pakuti kubwalo anacepsa khoma pozungulirapo, mitanda isalongedwe m'makoma a nyumba.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:6 nkhani