Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 6:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacinga makoma a nyumba m'katimo ndi matabwa amkungudza, kuyambira pansi kufikira posanja, nacinga m'katimo ndi matabwa, nayala pansi m'nyumbamo matabwa amlombwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:15 nkhani