Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika zitapita zaka mazana anai mphambu makumi asanu ndi atatu ataturuka ana a Israyeli m'dziko la Aigupto, caka cacinai cakukhala Solomo mfumu ya Israyeli, m'mwezi wa Zivi, ndiwo mwezi waciwiri, iye anayamba kumanga nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:1 nkhani