Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anapatsa Solomo nzeru monga momwe adamlonjezera; ndipo panali mtendere pakati pa Hiramu ndi Solomo, iwo awiri napangana pamodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:12 nkhani