Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anapatsa Hiramu miyeso ya tirigu zikwi makumi awiri ndiyo zakudya za banja lace, ndi miyeso makumi awiri ya mafuta oyera; motero Solomo anapatsa Hiramu caka ndi caka.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:11 nkhani