Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 4:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anali wanzeru woposa anthu onse, woposa Etani wa ku Ezra, ndi Hemani, ndi Kalikoli, ndi Darida ana a Maholi; ndipo mbiri yace inafikira amitundu onse ozungulira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 4

Onani 1 Mafumu 4:31 nkhani