Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anati, Munamcitira mtumiki wanu Davide atate wanga zokoma zazikulu, monga umo anayenda pamaso panu ndi coonadi ndi cilungamo ndi mtima woongoka ndi Inu; ndipo mwamsungira cokoma ici cacikuru kuti mwampatsa mwana kukhala pa mpando wace wacifumu monga lero lino.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:6 nkhani