Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pouka ine m'mawa kuyamwitsa mwana wanga ndaona ngwakufa, koma nditamzindikira m'mawa ndaona si mwana wanga wobala ine ai.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:21 nkhani