Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anauka, ndipo taona, ndilo loto; nabwera ku Yerusalemu, naima ku likasa la cipangano ca Yehova, napereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamtendere, nakonzera anyamata ace onse madyerero.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:15 nkhani