Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 21:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahabu analankhula ndi Naboti, nati, diloleni Ndipatse munda wako wamphesa ukhale munda wanga wa ndiwo, popeza uli pafupi ndi nyumba yanga; ndipo m'malo mwace ndidzakupatsa munda wamphesa wokoma woposa uwu; kapena kukakukomera ndidzakupatsa ndalama za pa mtengo wace,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:2 nkhani