Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 21:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atamva Ahabu kuti Naboti wafa, Ahabu anauka kukatsikira ku munda wamphesa wa Naboti, kuulandira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:16 nkhani